Numeri 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku limene anamanga chihema,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho. Koma kuyambira madzulo mpaka mʼmamawa, moto unkaoneka pamwamba pa chihemacho.+ Chivumbulutso 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
15 Pa tsiku limene anamanga chihema,+ mtambo unaima pamwamba pa chihema cha Umbonicho. Koma kuyambira madzulo mpaka mʼmamawa, moto unkaoneka pamwamba pa chihemacho.+