-
Salimo 105:34, 35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Analamula kuti pagwe dzombe,
Dzombe lingʼonolingʼono losawerengeka.+
35 Dzombelo linadya zomera zonse mʼdziko lawo,
Linadyanso mbewu zonse zamʼmunda mwawo.
-