-
Salimo 78:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa a ku Iguputo,+
Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka mʼmatenti a Hamu.
-
-
Salimo 105:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako Mulungu anapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko lawo,+
Chiyambi cha mphamvu zawo zobereka.
-
-
Salimo 136:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iye anapha ana oyamba kubadwa a Aiguputo,+
Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
-