-
Numeri 33:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mose ankalemba malo amene ankanyamukira ulendo uliwonse mogwirizana ndi zimene Yehova anamulamula. Awa ndi maulendo amene anayenda kuchokera kumalo ena kukafika kumalo ena:+
-