-
Salimo 78:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iwo anayesa Mulungu mʼmitima yawo+
Pomuumiriza kuti awapatse chakudya chimene ankalakalaka.
-
-
Salimo 78:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chifukwa chakuti sanakhulupirire Mulungu.+
Sanakhulupirire kuti iye angathe kuwapulumutsa.
-