Yoswa 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimene Yehova analamula mtumiki wake Mose, Mose analamula Yoswa+ ndipo Yoswayo anachitadi zonse. Palibe chilichonse chimene Yoswa sanachite pa zonse zimene Yehova analamula Mose.+
15 Zimene Yehova analamula mtumiki wake Mose, Mose analamula Yoswa+ ndipo Yoswayo anachitadi zonse. Palibe chilichonse chimene Yoswa sanachite pa zonse zimene Yehova analamula Mose.+