Yoswa 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova. Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova.
28 Ndiyeno anauza munthu kuti: ‘Tamvera, kuopa Yehova ndi nzeru,+Ndipo kupewa zoipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+