-
Deuteronomo 5:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Iweyo upite pafupi ukamvetsere zonse zimene Yehova Mulungu wathu akanene. Ndiyeno iweyo udzatiuze zonse zimene Yehova Mulungu wathu wakuuza, ndipo ife tidzamvera nʼkuchita zomwezo.’+
-