Deuteronomo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova anapereka malamulo* amenewa ku mpingo wanu wonse, mʼphiri. Analankhula mokweza kuchokera mʼmoto ndi mumtambo wakuda+ ndipo pa malamulowo sanawonjezerepo kalikonse. Kenako anawalemba pamiyala iwiri yosema nʼkundipatsa.+
22 Yehova anapereka malamulo* amenewa ku mpingo wanu wonse, mʼphiri. Analankhula mokweza kuchokera mʼmoto ndi mumtambo wakuda+ ndipo pa malamulowo sanawonjezerepo kalikonse. Kenako anawalemba pamiyala iwiri yosema nʼkundipatsa.+