-
Numeri 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 mwamunayo azitenga mkaziyo nʼkupita naye kwa wansembe. Azipita ndi nsembe ya mkaziyo ya ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa.* Ufawo asamauthire mafuta kapena lubani chifukwa ndi nsembe yambewu yansanje, nsembe yambewu yokumbutsa cholakwa.
-