Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa muzimupatula nʼkumupereka kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwiritse ntchito iliyonse mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe,* kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.

  • Deuteronomo 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma ngati nyamayo ili ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, musamaipereke nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+

  • Malaki 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Wotembereredwa ndi aliyense wochita zachinyengo, amene ali ndi nyama yabwinobwino yamphongo pa ziweto zake koma amalonjeza nʼkupereka nsembe nyama yachilema kwa Yehova. Ine ndine Mfumu yaikulu+ ndipo dzina langa lidzaopedwa pakati pa anthu a mitundu ina,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani