Levitiko 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, amene anamuthira mafuta odzozera unsembe pamutu pake,+ nʼkuikidwa kukhala wansembe* kuti azivala zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala ndipo asangʼambe zovala zake.+
10 Mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, amene anamuthira mafuta odzozera unsembe pamutu pake,+ nʼkuikidwa kukhala wansembe* kuti azivala zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala ndipo asangʼambe zovala zake.+