Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+ 2 Mbiri 17:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nehemiya 8:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.