-
Levitiko 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Nthawi yomweyo Aroni anapita kuguwa lansembe nʼkupha ngʼombe yaingʼono kuti ikhale nsembe yake+ yamachimo.
-
-
Levitiko 9:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Aroni anapha nyama ya nsembe yopsereza ndipo ana ake anamupatsa magazi a nyamayo. Atatero iye anawaza magaziwo mbali zonse za guwa lansembe.+
-