Deuteronomo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake molakwika osamulanga.+
11 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake molakwika osamulanga.+