-
Numeri 1:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Anthu onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+
-
-
Numeri 1:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 “Anthu a fuko la Levi okha usawalembe mayina, ndipo usaphatikize chiwerengero chawo pamodzi ndi cha Aisiraeli enawo.+
-