Numeri 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana a Merari, potengera mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Mabanja a Alevi anali amenewa potengera nyumba za makolo awo. 1 Mbiri 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
20 Ana a Merari, potengera mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Mabanja a Alevi anali amenewa potengera nyumba za makolo awo.