Numeri 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo musaiwale Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,+ chifukwa sanapatsidwe gawo kapena cholowa ngati inuyo.+ Yoswa 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mose anali atagawira kale cholowa mafuko awiri ndi hafu kutsidya lina la Yorodano.*+ Koma Alevi sanawagawire cholowacho.+
27 Ndipo musaiwale Mlevi amene akukhala mumzinda wanu,+ chifukwa sanapatsidwe gawo kapena cholowa ngati inuyo.+
3 Mose anali atagawira kale cholowa mafuko awiri ndi hafu kutsidya lina la Yorodano.*+ Koma Alevi sanawagawire cholowacho.+