Numeri 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
14 Panadutsa zaka 38 kuti tiyende kuchokera ku Kadesi-barinea nʼkuwoloka chigwa cha Zeredi,* mpaka mʼbadwo wonse wa amuna opita kunkhondo utatha pakati pathu, mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa iwo.+