Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 14:29, 30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mitembo yanu idzagona mʼchipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ 30 Nonsenu simudzalowa mʼdziko limene ndinalumbira* kuti mudzakhalamo,+ kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+

  • Yoswa 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yoswa 19:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Choncho anamaliza kugawa dzikolo ndipo fuko lililonse linali ndi cholowa chake. Kenako Aisiraeli anamʼpatsa Yoswa mwana wa Nuni cholowa chake pakati pawo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani