-
Numeri 14:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ine Yehova ndalankhula. Zimene ndidzachitire gulu lonse la anthu oipali, amene asonkhana kuti atsutsane ndi ine ndi izi: Onse adzafera mʼchipululu muno ndipo adzathera momwe muno.+
-