-
Yoswa 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Tidzamvera chilichonse chimene mungatiuze ngati mmene tinkachitira ndi Mose. Yehova Mulungu wanu akhale nanu ngati mmene anakhalira ndi Mose.+
-