Ekisodo 29:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 munthu amene akupereka nsembeyo, azikaperekanso kwa Yehova nsembe yambewu ya ufa wosalala+ wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa.* Ufawo uzikakhala wothira mafuta okwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini.*
4 munthu amene akupereka nsembeyo, azikaperekanso kwa Yehova nsembe yambewu ya ufa wosalala+ wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa.* Ufawo uzikakhala wothira mafuta okwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini.*