-
Levitiko 23:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kwa masiku 7, muzipereka kwa Yehova nsembe zowotcha pamoto. Pa tsiku la 7 muzichita msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.’”
-
-
Deuteronomo 16:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Muzidya mkate wopanda zofufumitsa kwa masiku 6, ndipo pa tsiku la 7 muzichitira Yehova Mulungu wanu msonkhano wapadera. Pa tsikuli musamagwire ntchito.+
-