-
Levitiko 23:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pa tsiku limeneli muzilengeza+ kuti kuli msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale mʼmibadwo yanu yonse.
-