-
Levitiko 23:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 “Lankhula ndi Aisiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mʼmwezi wa 7, pa tsiku loyamba la mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, ndipo lipenga likalira+ muzisonkhana kuti mulambire Mulungu. 25 Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa pa tsikuli, ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova.’”
-