-
Deuteronomo 15:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma ngati nyamayo ili ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, musamaipereke nsembe kwa Yehova Mulungu wanu.+
-
-
Deuteronomo 17:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Musamapereke kwa Yehova Mulungu wanu nsembe ya ngʼombe kapena nkhosa imene ili ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa idzakhala yonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+
-