-
Salimo 94:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+
Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!
-
-
Yesaya 1:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,
Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti:
“Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,
Ndipo ndidzabwezera adani anga.+
-