Numeri 27:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Kwera phiri ili la Abarimu,+ ukaone dziko limene ndidzalipereke kwa Aisiraeli.+ 13 Ukaliona dzikolo, iwenso udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako*+ komanso Aroni mchimwene wako,+ Deuteronomo 32:48-50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Kwera phiri ili la Abarimu,+ ukaone dziko limene ndidzalipereke kwa Aisiraeli.+ 13 Ukaliona dzikolo, iwenso udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako*+ komanso Aroni mchimwene wako,+