-
Numeri 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, aziphedwa kuti asakhalenso mumpingowo,+ chifukwa wadetsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera, choncho ndi wodetsedwa.
-