Numeri 33:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kenako ananyamuka ku Alimoni-dibilataimu, nʼkukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+
47 Kenako ananyamuka ku Alimoni-dibilataimu, nʼkukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+