-
Deuteronomo 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pa nthawi imeneyo ndinakulamulani kuti: ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna onse olimba mtima atenge zida ndipo awoloke patsogolo pa abale anu, Aisiraeli.+
-