-
Deuteronomo 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mbali yotsala ya dera la Giliyadi ndi Basana yense amene anali mu ufumu wa Ogi ndinaipereka kwa hafu ya fuko la Manase.+ Dera lonse la Arigobi, limene ndi mbali ya Basana linkadziwika kuti ndi dziko la Arefai.
-