Numeri 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malo amenewo anawatchula kuti Kibiroti-hatava,*+ chifukwa anakwirirapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+ Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuwonjezera pamenepo, munaputanso mkwiyo wa Yehova ku Tabera,+ ku Masa+ ndi ku Kibiroti-hatava.+
34 Malo amenewo anawatchula kuti Kibiroti-hatava,*+ chifukwa anakwirirapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+