-
Numeri 21:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako anasamuka ku Oboti nʼkukamanga msasa ku Iye-abarimu,+ mʼchipululu choyangʼanizana ndi dziko la Mowabu, chakumʼmawa.
-
-
Numeri 21:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Atasamuka kumeneko anakamanga msasa mʼdera la chigwa cha Arinoni, mʼchipululu chochokera kumalire a dziko la Aamori. Chigwa cha Arinoni+ chinali malire pakati pa dziko la Mowabu ndi la Aamori.
-