Deuteronomo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene Wamʼmwambamwamba anapereka cholowa ku mitundu ya anthu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,*+Anaika malire a anthu ena onse+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+
8 Pamene Wamʼmwambamwamba anapereka cholowa ku mitundu ya anthu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,*+Anaika malire a anthu ena onse+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+