-
Deuteronomo 4:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Anachotsa pamaso panu mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, kuti akulowetseni mʼdziko lawo nʼkukupatsani kuti likhale cholowa chanu ngati mmene zilili lero.+
-
-
Yoswa 14:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+
-