Numeri 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 33:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yoswa 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pogawa cholowacho kwa mafuko 9 ndi hafu,+ anachita maere+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose. Yoswa 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pachovala,+Koma zonse zimene maerewo asonyeza zimachokera kwa Yehova.+
2 Pogawa cholowacho kwa mafuko 9 ndi hafu,+ anachita maere+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.