-
Numeri 3:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera.
-
-
Yoswa 14:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+
-