Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 34:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mutenge mtsogoleri mmodzi pa fuko lililonse kuti akathandize kugawa malowo kuti akhale cholowa chanu.+

  • Deuteronomo 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Pamene Wamʼmwambamwamba anapereka cholowa ku mitundu ya anthu,+

      Pamene analekanitsa ana a Adamu,*+

      Anaika malire a anthu ena onse+

      Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+

  • Yoswa 19:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Zimenezi zinali zigawo za cholowa chimene wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a Isiraeli anagawira anthu.+ Anagawa dzikolo pochita maere ku Silo+ pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako.+ Choncho anamaliza kugawa dzikolo.

  • Machitidwe 17:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani