Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Genesis 49:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Deuteronomo 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+

  • Yoswa 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yosefe anali mafuko awiri,+ la Manase ndi la Efuraimu.+ Alevi sanapatsidwe cholowa cha malo koma anangowapatsa mizinda+ yoti azikhalamo komanso malo odyetserako ziweto ndi osungirako katundu wawo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani