-
Numeri 26:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Amene ali ndi anthu ambiri apatsidwe dziko lalikulu monga cholowa chake, ndipo amene ali ndi anthu ochepa apatsidwe dziko lalingʼono monga cholowa chake.+ Aliyense apatsidwe cholowacho mogwirizana ndi chiwerengero cha anthu ake.
-