Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 4:41-43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Pa nthawi imeneyo, Mose anapatula mizinda itatu mbali yakumʼmawa kwa Yorodano.+ 42 Ngati munthu wapha mnzake mwangozi ndipo sanayambe wadanapo naye,+ munthu ameneyu azithawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi kuti akhale ndi moyo.+ 43 Mizinda yake ndi Bezeri,+ mʼchipululu chimene chili mʼdera lokwererapo, woti anthu a fuko la Rubeni azithawirako. Mzinda wa Ramoti+ ku Giliyadi, woti anthu a fuko la Gadi azithawirako ndi mzinda wa Golani+ ku Basana, woti anthu a fuko la Manase+ azithawirako.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani