-
Numeri 36:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zimene Yehova walamula zokhudza ana aakazi a Tselofekadi nʼzakuti: ‘Iwo angakwatiwe ndi aliyense amene angamukonde. Koma ayenera kukwatiwa ndi amuna a fuko la makolo awo okha.
-