-
Numeri 33:50Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Yehova analankhula ndi Mose ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, mʼchipululu cha Mowabu. Anamuuza kuti:
-
-
Numeri 35:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose mʼchipululu cha Mowabu ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano+ kuti:
-