Numeri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mukamasamutsa msasa, Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihema nʼkuchotsa katani+ ndipo aziphimba likasa+ la Umboni ndi kataniyo.
5 Mukamasamutsa msasa, Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihema nʼkuchotsa katani+ ndipo aziphimba likasa+ la Umboni ndi kataniyo.