-
Deuteronomo 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho ndinatenga atsogoleri a mafuko anu, amuna anzeru ndi ozindikira nʼkuwaika kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50, atsogoleri a magulu a anthu 10 ndi akapitawo a mʼmafuko anu.+
-