Numeri 26:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mliri uja utatha,+ Yehova anauza Mose ndi Eleazara mwana wa wansembe Aroni kuti: 2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+
26 Mliri uja utatha,+ Yehova anauza Mose ndi Eleazara mwana wa wansembe Aroni kuti: 2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+