-
Numeri 3:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ana a Kohati, potengera mabanja awo, anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+
-
-
Numeri 3:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mabanja a Aamuramu, Aizara, Aheburoni ndi Auziyeli anachokera mwa Kohati.+ Amenewa ndi amene anali mabanja a Akohati.
-