-
Numeri 4:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 “Uwerenge ana onse a Gerisoni+ potengera nyumba za makolo awo komanso mabanja awo. 23 Muwerenge onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.
-